Zamkatimu
May 1, 2010
Kodi Mulungu Watinyanyala?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Mulungu Sakuona Zikuchitikazi?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
14 Zoti Achinyamata Achite—Khalani Olimba Mtima Potsatira Zimene Mumakhulupirira
16 Zimene Tikuphunzira kwa Yesu—Zimene Tingachite Kuti Titsatire Khristu
18 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Kuphunzitsa Ana Kuti Adzathe Kudziimira Paokha
30 Yandikirani Mulungu—Amakhululukira Munthu wa “Mtima Wosweka ndi Wolapa”
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
8 Kodi Amuna ndi Akazi Amasiye Amafunikira Chiyani? Nanga Mungawathandize Bwanji?
21 Dzina la Mulungu Lakuti Yehova, Linapezeka M’kachisi wa ku Iguputo
23 “Uthenga Wabwino” Ukulalikidwa Kuzilumba Zakumpoto kwa Australia