Zamkatimu
June 1, 2010
N’chifukwa Chiyani Anthu Sakuopanso Kuchita Tchimo?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
4 Kodi Chasintha N’chiyani pa Nkhani ya Tchimo?
8 Dziwani Zoona Zake pa Nkhani ya Tchimo
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Kalata Yochokera ku South Africa
24 Phunzitsani Ana Anu —Anthu Amene Analemba za Yesu
26 Yandikirani Mulungu —“Mudzakhala Wokhulupirika”
27 Zimene Owerenga Amafunsa . . .
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
11 Kodi Kuchita Zimenezi N’kusaonadi Mtima?
18 Kodi Nyenyezi Zingakuthandizeni pa Moyo Wanu?
21 Mafuta a Basamu wa ku Gileadi Ndi Ochiritsa
28 Kodi Anali Kuikiradi Chikhristu Kumbuyo Kapena Ankaphunzitsa Nzeru za Anthu?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
NASA, ESA, and A. Nota (STScI)