Zamkatimu
October 1, 2010
Mfundo 7 Zimene Muyenera Kudziwa pa Nkhani ya Pemphero
NKHANI ZOYAMBIRIRA
Mfundo 7 Zimene Muyenera Kudziwa pa Nkhani ya Pemphero
3 Kodi N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera?
4 Kodi Tiyenera Kupemphera kwa Ndani?
6 Kodi Tiyenera Kupemphera Bwanji?
7 Kodi Tiyenera Kupemphera za Chiyani?
9 Kodi Tiyenera Kupemphera Pamalo Ati, Nanga Nthawi Yanji?
10 Kodi Kupemphera N’kothandiza?
11 Kodi Mulungu Amamva ndi Kuyankha Mapemphero?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
14 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—“Anapitiriza Kukula, Akukondedwa ndi Yehova”
23 Yandikirani Mulungu—“Wakumva Pemphero”
24 Phunzitsani Ana Anu—Ufumu Umene Udzasintha Dziko Lonse Lapansi
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
19 Kodi Mungatani Kuti Musamangokhala Wankhawa Ndiponso Wachisoni?
26 Kucheza ndi Mnzathu—Kodi Mzimu Woyera N’chiyani?
29 Kodi Masiku ano Mulungu ndi Amene Amachititsa Anthu Kulankhula Malilime?