Zamkatimu
February 1, 2011
Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Lolimba?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 N’chifukwa Chiyani Mabanja Ambiri Akutha?
4 Malangizo Othandiza pa Zimene Amuna Komanso Akazi Ambiri Amadandaula
• “Palibenso phindu lililonse limene ndikupeza m’banja”
• “Mwamuna (kapena mkazi) wanga sachita zimene amayenera kuchita”
• “Mwamuna wanga sachita zinthu ngati mwamuna”
• “Zimene mwamuna (kapena mkazi) wanga amachita zimandikwiyitsa ndipo zanditopetsa”
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
14 Yandikirani Mulungu—“Inu Mulungu Wanga, Mundikumbukire pa Zabwino Zimene Ndinachita”
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Mulungu Ndani?
18 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Muziphunzitsa Ana Anu Makhalidwe Abwino
25 Phunzitsani Ana Anu—Ankakondedwa ndi Mulungu Komanso Anzake
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
21 Kodi Mukukonzekera Tsiku Lofunika Kwambiri Chaka Chino?
28 “Lero Ndi Tsiku Limene Mwakhala Mukuliyembekezera”