Zamkatimu
October 1, 2011
Zimene Baibulo Limanena pa Zikhulupiriro Zisanu Zabodza Zokhudza Mulungu
NKHANI ZOYAMBIRIRA
4 Mulungu Ndi Wosamvetsetseka—Kodi Zimenezi Ndi Zoona?
5 Mulungu Satidera Nkhawa—Kodi Zimenezi Ndi Zoona?
6 Mulungu Amakonda Kulanga Amene Amulakwira—Kodi Zimenezi Ndi Zoona?
7 Mulungu Amachita Zinthu Mopanda Chilungamo—Kodi Zimenezi Ndi Zoona?
8 Mulungu Amavomereza Zipembedzo Zonse—Kodi Zimenezi Ndi Zoona?
9 Kudziwa Zoona Kungasinthe Moyo Wanu
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
15 Yandikirani Mulungu—Mukhoza ‘Kumudziwadi Mulungu’
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Losangalala?
18 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
24 Phunzitsani Ana Anu—Nthawi Imene Sitiyenera Kugona
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
14 “Anthu Olimba Mtima Ofunika Kuwayamikira”