Zamkatimu
November 1, 2011
Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani Yokhudza Kugonana
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi N’chifukwa Chiyani Kudziwa Zimenezi Kuli Kofunika?
4 Mayankho a Mafunso 10 Okhudza Kugonana
8 Kodi N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutsatira Mfundo za M’Baibulo?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
13 Chinsinsi cha Banja Losangalala—Yesetsani Kuti Banja Lanu Lizikonda Zinthu Zauzimu
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Malamulo a Mulungu Amatithandiza Bwanji?
21 Yandikirani Mulungu—Kukwaniritsa Udindo Wathu kwa Mulungu
30 Zoti Achinyamata Achite—Anapulumutsidwa M’ng’anjo Yoyaka Moto
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
18 Kodi Bambo Angatani Kuti Azigwirizana Kwambiri Ndi Mwana Wake Wamwamuna?
22 Kodi Yerusalemu Wakale Anawonongedwa Liti?—Kodi Zolemba za Pamapale Akale Zimasonyeza Chiyani?