Zamkatimu
December 1, 2011
Kodi Masoka Achilengedwe N’chilango Chochokera kwa Mulungu?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
4 N’chifukwa Chiyani Masoka Achilengedwe Achuluka Chonchi?
6 Zimene Mungachite Kuti Musavutike Kwambiri ndi Masoka Achilengedwe
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Tingapeze Bwanji Anzathu Abwino?
26 Yandikirani Mulungu—“Woyera, Woyera, Woyera Ndiye Yehova”
30 Phunzitsani Ana Anu—Ankatchedwa “Ana a Bingu”
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
11 Kodi Ndani Angamasulire Ulosi?
18 Alfonso de Zamora Anayesetsa Kumasulira Malemba Molondola Ndipo Anagwiritsa Ntchito Dzina la Mulungu
23 “Nthawi ya Chikondi ndi Nthawi ya Chidani”
27 Ndinkafuna Kukhala Ngati Mwana wa Yefita