Zamkatimu
April 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino ndi wathu.
Mayankho a Mafunso Onena za Yesu Khristu
NKHANI ZOYAMBIRIRA
4 Mayankho a Mafunso Onena za Yesu Khristu
8 Kodi Kudziwa Mayankho Olondola Kuli Ndi Phindu?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
10 Yandikirani Mulungu—“Ndithandizeni Kubwerera”
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi N’chifukwa Chiyani Akhristu Amabatizidwa?
29 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Ndani Anatumiza Nyenyezi Imene Inatsogolera Anthu Kwa Yesu?
30 Zoti Achinyamata Achite—Mose Anapatsidwa Ntchito Yapadera
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
18 Kodi Pali Mabuku Ena a Uthenga Wabwino Amene Amafotokoza Nkhani za Yesu Zimene M’Baibulo Mulibe?
20 Kucheza ndi Mnzathu—Kodi Yesu Ndi Mulungu?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photo credits pages 2 and 3, clockwise from top left: © Massimo Pizzotti/age fotostock and Hagia Sophia; © Angelo Cavalli/age fotostock; © Alain Caste/age fotostock; © 2010 SuperStock; Engravings by Doré