Zamkatimu
July 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Ndani Amamvetsera Mukamapemphera?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Pali Aliyense Amene Amamvetsera Tikamapemphera?
4 Kodi Ndani Amamva Mapemphero Athu?
6 N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
18 Yandikirani Mulungu—Kodi Mulungu Akakhululuka Machimo, Samawakumbukiranso?
23 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—“Kumene Inu Mupite Inenso Ndipita Komweko”
30 Zoti Achinyamata Achite—Mulungu Amadana Ndi Zinthu Zopanda Chilungamo
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IYI: