Zamkatimu
August 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Zozizwitsa Zimachitikadi?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 N’chifukwa Chiyani Nkhani Yokhudza Zozizwitsa Ili Yofunika Kuidziwa Bwino?
4 Kodi Zozizwitsa Zimachitikadi?—Mfundo Zitatu Zimene Anthu Amene Samakhulupirira Zozizwitsa Amanena
7 Umboni Woti Zozizwitsa Zotchulidwa M’Baibulo Zinachitikadi
8 Zozizwitsa Zimene Zichitike Posachedwapa
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
15 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Mulungu Amaona Kuti N’kulakwa Kusuta Fodya?
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Yesu Anakhala Liti Mfumu?
24 Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
27 Yandikirani Mulungu—Yehova Amadana ndi Zinthu Zopanda Chilungamo
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
18 Moyo wa Anthu Akale—Msodzi
21 Kucheza Ndi Munthu Wina—Kodi Anthu Onse Abwino Amapita Kumwamba?