Zamkatimu
October 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Ziphuphu Zidzatha?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
4 N’chifukwa Chiyani Anthu Akupitirizabe Kuchita Ziphuphu?
5 Kodi N’zotheka Kuchita Zinthu Mwachilungamo M’dziko Laziphuphuli?
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi N’zotheka Kukhala Ndi Moyo Kwamuyaya?
18 Yandikirani Mulungu—“Wamasiku Ambiri Anakhala pa Mpando”
19 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Anali “Mkazi Wabwino Kwambiri”
25 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Banja Ndi Limene Limapangitsa Munthu Kukhala Wosangalala?
30 Zoti Achinyamata Achite—Pewani Mtima Wofuna Kutchuka
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
9 Mmene Mawu a Mulungu Anathandizira Banja Lathu Lachihindu
12 Kucheza ndi Munthu Wina—Kodi Mulungu Amalanga Anthu Kumoto?