Zamkatimu
December 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Pali Zina Zosangalatsa Kuposa Khirisimasi
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Zimene Ena Amachita pa Khirisimasi Pofuna Kusangalala
9 Amasangalala Ngakhale Kuti Sachita Khirisimasi
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
10 Zimene Owerenga Amafunsa—N’chifukwa Chiyani Anthu Ena Sachita Nawo Khirisimasi?
11 Yandikirani Mulungu—Kodi Dzina Lanu Lili ‘M’buku la Chikumbutso’ la Mulungu?
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—N’chifukwa Chiyani Mulungu Anatumiza Yesu Padziko Lapansi?
30 Phunzitsani Ana Anu—Yotamu Anakhalabe Wokhulupirika Bambo Ake Atasiya Kutumikira Yehova
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
12 Nditavutika kwa Zaka Zambiri, Ndinapeza Ufulu Weniweni
18 Kodi Mumakhulupirira Kuti Musanabadwe Munakhalapo ndi Moyo Kwinakwake?
24 Zodzoladzola Zimene Anthu Akale Ankagwiritsa Ntchito Podzikongoletsa