Zamkatimu
January 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
NKHANI YA PACHIKUTO: KODI MUYENERA KUOPA KUTHA KWA DZIKOLI?
Nkhani ya Kutha kwa Dziko, Kodi Ndi Yoopsa, Yosangalatsa Kapena Yokhumudwitsa? 4
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
Yandikirani Mulungu—“Mwaziulula kwa Tiana” 9
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—“Ngakhale Kuti Anafa, Iye Akulankhulabe” 12
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI IYI | www.jw.org
ZOTI ACHINYAMATA ACHITE—Pewani Nsanje
Phunzirani zimene zinachitika Miriamu ndi Aroni atayamba kuchitira nsanje mchimwene wawo, Mose.
(Onani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ACHINYAMATA)
ZIMENE NDIKUPHUNZIRA M’BAIBULO
Thandizani ana anu aang’ono kuzindikira kufunika konena kuti, “zikomo kwambiri.”
(Onani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA/ANA)