Zamkatimu
October 1, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Baibulo Lili Ndi Uthenga Wotani?
TSAMBA 3 MPAKA 7
N’chifukwa Chiyani Mukufunika Kulidziwa Bwino Baibulo? 3
Zimene Zinachitika Kuti Tizikumana ndi Mavuto 4
Mulungu Akonza Zopulumutsa Anthu 5
Uthenga Wabwino Wopita ku Mitundu Yonse 7
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
Zimene Mungachite Ngati Banja Lanu Latha 8
Yandikirani Mulungu—“Yehova Anakukhululukirani ndi Mtima Wonse” 11
Kodi Kaonekedwe ka Zinthu Kamakukhudzani Bwanji? 14
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAPEZE ZAMBIRI PA WEBUSAITI YA | www.jw.org
MAFUNSO AMENE ANTHU AMAKONDA KUFUNSA KAWIRIKAWIRI OKHUDZA MBONI ZA YEHOVA—N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?
(Fufuzani pa mawu akuti NKHANI ZOKHUDZA MBONI ZA YEHOVA > MAFUNSO AMENE ANTHU AMAFUNSA KAWIRIKAWIRI)