Zamkatimu
August 1, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
NKHANI YA PACHIKUTO
Kodi Mulungu Amakuonani Kuti Ndinu Wofunika?
TSAMBA 3 MPAKA 7
Kodi Mulungu Amakuganizirani? 3
Mulungu Amaona Zomwe Zikuchitika pa Moyo Wanu 4
Mulungu Angakulimbikitseni ndi Kukuthandizani 6
Mulungu Akufuna Kuti Mukhale Naye pa Ubwenzi 7
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—“Tamverani Maloto Amene Ine Ndinalota” 10
Zimene Owerenga Amafunsa . . . Kodi Ndani Analenga Mulungu? 15
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo 16
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZINA PA WEBUSAITI YATHU YA | www.pr418.com
MUNGAPEZE YANKHO LA M’BAIBULO LA FUNSO ILI—Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?
(Fufuzani pa mawu akuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA >KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)