Zamkatimu
Na. 1, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
KODI INUYO MUKUGANIZA BWANJI?
Kodi mukuona kuti padzikoli bwenzi zinthu zikuyenda bwino zikanakhala kuti anthu amatsatira mfundo ya m’Baibulo iyi?
“Tikufuna kuchita zinthu zonse moona mtima.”—Aheberi 13:18.
Magaziniyi yafotokoza kufunika kopewa zachinyengo
NKHANI YA PACHIKUTO
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuchita Zinthu Moona Mtima?
Kodi Kukhala Oona Mtima N’kwachikale? 3
Kodi Chinyengo N’choopsa Bwanji? 4
Kodi Ubwino Wopewa Chinyengo Ndi Wotani? 6
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
N’chiyani Chingakuthandizeni Kuti Musamakhale Mwamantha? 11
Kodi Baibulo Limanena Zotani? 16
MUNGAWERENGENSO NKHANI ZINA PA WEBUSAITI YATHU
(Pitani pamene palembedwa kuti, ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBULO)