Magazini Yophunzira
March 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA: MAY 2-29, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
BELGIUM
Nyumba ya Ufumu ya ku Wijnegem ili m’mphepete mwa msewu waukulu kwambiri ku Antwerp. Chikwangwani cha JW.ORG chinaikidwa kungoyambira pamene anayamba kumanga nyumbayi
KULI ANTHU
11,132,269
KULI OFALITSA
25,839
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2014)
44,635
Magaziniyi sitigulitsa. Timapereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa www.pr418.com.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.