Magazini Yophunzira
MAY 2016
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: JUNE 27 MPAKA JULY 31, 2016
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
GHANA
Wofalitsa Ufumu wakhama akulalikira kwa ana a sukulu anzake pogwiritsa ntchito kapepala. Mtsikanayu amakhala m’tauni ya Ho m’chigawo cha Volta ku Ghana
KULI OFALITSA
125,443
MAPHUNZIRO A BAIBULO
382,408
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2014)
347,725
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.