Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA AUGUST 1-7, 2016
6 Tiziyamikira Kuti Yehova Amatiumba
MLUNGU WA AUGUST 8-14, 2016
11 Kodi Mumalola Kuti Yehova Azikuumbani?
Munthu akamaumba chinthu, amakhala nacho pafupi kwambiri. M’nkhani ziwirizi, tiona mmene Yehova amatiumbira komanso zimene tingachite kuti tikhale ngati dongo labwino.
16 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
MLUNGU WA AUGUST 15-21, 2016
18 “Yehova Mulungu Wathu Ndi Yehova Mmodzi”
Kodi mawu oti Yehova Mulungu wathu ndi “Yehova mmodzi” amatanthauza chiyani? Nanga zimenezi zimakhudza bwanji ubwenzi wathu ndi iye komanso ndi Akhristu anzathu? Popeza m’dzikoli muli anthu amitundu komanso zikhalidwe zosiyanasiyana, tiyenera kumvetsa bwino zimene Yehova amafuna kuti tizichita n’cholinga choti akhale “Mulungu wathu.”
MLUNGU WA AUGUST 22-28, 2016
23 Tisasiye Kutumikira Mulungu Chifukwa cha Zochita za Ena
Tonsefe nthawi zina timakhumudwitsa anzathu. Kodi ndi zitsanzo za m’Baibulo ziti zomwe zingatithandize kudziwa zoyenera kuchita ena akalankhula kapena kuchita zinthu zotikhumudwitsa?