Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
MLUNGU WA OCTOBER 24-30, 2016
MLUNGU WA OCTOBER 31, 2016–NOVEMBER 6, 2016
8 Pitirizani Kulimbana ndi Zimene Zingakulepheretseni Kupeza Madalitso
Akhristufe tikhoza kuda nkhawa komanso kukumana ndi mavuto ena. Nkhanizi zikusonyeza kuti dzanja lamphamvu la Yehova lingatithandize kuti tithe kupirira. Tionanso zimene tingachite kuti chilichonse chisatilepheretse kupeza madalitso.
13 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
14 Paulo Anateteza Uthenga Wabwino kwa Akuluakulu a Boma
MLUNGU WA NOVEMBER 7-13, 2016
17 Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu?
Atumiki a Yehovafe timafuna kuti tizivala zovala zaukhondo, zogwirizana ndi kumene tikukhala komanso zosasemphana ndi mfundo za m’Malemba. Kodi tingatani kuti zovala zathu zizilemekeza Mulungu?
22 Muzilola Kuti Yehova Azikutsogolerani
MLUNGU WA NOVEMBER 14-20, 2016
23 Achinyamata, Yesetsani Kulimbitsa Chikhulupiriro Chanu
MLUNGU WA NOVEMBER 21-27, 2016
28 Muzithandiza Ana Anu Kuti Akhale Ndi Chikhulupiriro Cholimba
M’nkhani ziwirizi tiona zimene achinyamata angachite kuti akhale ndi chikhulupiriro cholimba komanso kuti azitha kufotokozera anthu ena zimene amakhulupirira. Tionanso zimene makolo angachite kuti ana awo azisangalala pophunzira Mawu a Mulungu n’cholinga choti akhale ndi chikhulupiriro cholimba.