Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp17 No. 1 tsamba 1-2
  • Kodi Mungatani Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzikusangalatsani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungatani Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzikusangalatsani?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2017
wp17 No. 1 tsamba 1-2
Magazini a Nsanja ya Olonda, Na. 1, 2017 | Kodi Mungatani Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzikusangalatsani?

Kodi Mungatani Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzikusangalatsani?

Na. 1 2017

© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.

Ngati mukufuna kupereka ndalama zothandizira pa ntchito yolalikira, pitani pa www.pr418.com.

Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.

MAGAZINI ya Nsanja ya Olonda imalemekeza Yehova Mulungu, yemwe ndi Wolamulira wa chilengedwe chonse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti Ufumu wa Mulungu posachedwapa uchotsa zoipa zonse n’kusintha dziko lapansili kukhala paradaiso. Imalimbikitsa anthu kukhulupirira Yesu Khristu yemwe anatifera kuti tipeze moyo wosatha ndipo panopo akulamulira monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambira mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zimachokera m’Baibulo.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena