Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w17 January tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
w17 January tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse

MLUNGU WA FEBRUARY 27, 2017–MARCH 5, 2017

7 “Khulupirira Yehova Ndipo Chita Zabwino”

Nkhaniyi ikufotokoza lemba la chaka cha 2017 lomwe likutilimbikitsa kudalira Yehova tikakumana ndi mavuto. Tiona zitsanzo zakale zotithandiza kuti tizidalira Yehova, uku tikuchita zonse zimene tingathe pothana ndi mavuto athu komanso pothandiza ena.

MLUNGU WA MARCH 6-12, 2017

12 Ufulu Wosankha Zochita Ndi Mphatso Yapadera

M’nkhaniyi, tiona zimene tingachite poyamikira mphatso ya ufulu wosankha zochita imene Mulungu anatipatsa. Tionanso zimene tingachite kuti tiziigwiritsa ntchito bwino. Nkhaniyi itithandizanso kuti tizilemekeza ufulu wa ena wosankha zochita.

MLUNGU WA MARCH 13-19, 2017

17 Kudzichepetsa N’kofunika Kwambiri

MLUNGU WA MARCH 20-26, 2017

22 Kodi Tingatani Kuti Nthawi Zonse Tizikhala Odzichepetsa?

Nkhani zimenezi zitithandiza kumvetsa bwino khalidwe la kudzichepetsa. Nkhani yoyamba ikufotokoza zimene kudzichepetsa kumatanthauza komanso zimene sikutanthauza. Nkhani yachiwiri itithandiza kudziwa zimene tingachite kuti nthawi zonse tizikhala odzichepetsa.

MLUNGU WA MARCH 27, 2017–APRIL 2, 2017

27 ‘Zinthu Zimenezo Uziziphunzitsa kwa Anthu Okhulupirika’

Abale audindo akamakula pamafunika ena achinyamata oti azigwira ntchito zimene achikulirewo ankagwira. Nkhaniyi ikufotokoza zimene abale achikulire komanso achinyamata angachite kuti zinthu ziziyenda bwino.

32 Kodi Mukudziwa?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena