Magazini Yophunzira
FEBRUARY 2017
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA APRIL 3-30, 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
PATSAMBA LOYAMBA:
ETHIOPIA
M’bale akugwiritsa ntchito Baibulo polalikira uthenga wa Ufumu kwa azibambo awiri kudera lamapiri, ku Ethiopia. Azibambowo afundira nsalu zomwe ndi zofala kuderali
KULI ANTHU
99,391,000
OFALITSA
10,083
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO (2015)
25,323
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka, pitani pawebusaiti yathu ya www.jw.org/ny.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.