Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w17 March tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
w17 March tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

3 Mbiri ya Moyo Wanga​—Kuyenda Ndi Anthu Anzeru Kwandithandiza Kwambiri

MLUNGU WA MAY 1-7, 2017

8 Tizipereka Ulemu kwa Oyenera Kulemekezedwa

Akhristu ayenera kudziwa malire pa nkhani yopereka ulemu. Kodi ndi ndani amene tiyenera kuwapatsa ulemu, nanga n’chifukwa chiyani? M’nkhaniyi tipeza yankho la funso limeneli. Ikufotokozanso ubwino wopereka ulemu kwa anthu oyenera kulemekezedwa.

MLUNGU WA MAY 8-14, 2017

13 Muzikhulupirira Yehova Kuti Muzisankha Zochita Mwanzeru

Baibulo limasonyeza kuti tiyenera kusankha zochita osati kumangokayikakayika. Koma kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kusankha zochita mwanzeru, nanga n’chiyani chingatithandize? Kodi ndi bwino kusintha zimene tinasankha? Nkhaniyi itithandiza kuyankha mafunso amenewa.

MLUNGU WA MAY 15-21, 2017

18 Tizitumikira Yehova ndi Mtima Wathunthu

MLUNGU WA MAY 22-28, 2017

23 Kodi Mumatsatira Ndi Mtima Wonse Zimene Zinalembedwa?

Popeza si ife angwiro, timalakwitsa zinthu zina. Koma kodi izi zikutanthauza kuti sitingasangalatse Yehova? M’nkhanizi tikambirana zitsanzo za mafumu 4 a ku Yuda ndipo tionanso zimene analakwitsa. Koma Yehova ankaona kuti mafumu onsewo ankamutumikira ndi mtima wathunthu. Kodi iye angaonenso kuti ifeyo timamutumikira ndi mtima wathunthu ngakhale kuti timalakwitsa zinthu zina?

28 Kodi Mumakhalabe Bwenzi Labwino Zinthu Zikavuta?

32 Dzina la M’Baibulo Linapezeka Pamtsuko Wakale

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena