Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w17 December tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
w17 December tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

MLUNGU WA JANUARY 29, 2018–FEBRUARY 4, 2018

3 “Ndikudziwa Kuti Adzauka”

MLUNGU WA FEBRUARY 5-11, 2018

8 “Ndili ndi Chiyembekezo mwa Mulungu”

Kodi ndi nkhani ziti za m’Baibulo zimene zinathandiza Akhristu kukhulupirira kuti akufa adzauka? Kodi nkhanizo komanso zimene anthu ena akale ankakhulupirira pa nkhaniyi zingakuthandizeni bwanji kukhala ndi chiyembekezo? Nkhani ziwirizi zikuthandizani kukhulupirira kwambiri kuti akufa adzauka.

13 Kodi Mukukumbukira?

14 Mafunso Ochokera kwa Owerenga

16 Mafunso Ochokera kwa Owerenga

MLUNGU WA FEBRUARY 12-18, 2018

18 Makolo, Thandizani Ana Anu Kupeza Nzeru Kuti Adzapulumuke

MLUNGU WA FEBRUARY 19-25, 2018

23 Achinyamata, “Pitirizani Kukonza Chipulumutso Chanu”

Pa anthu masauzande ambiri amene amabatizidwa chaka chilichonse pamakhala achinyamata ambiri. Munthu akabatizidwa amadalitsidwa kwambiri koma amakhalanso ndi udindo waukulu. Ngati ndinu makolo, kodi mungathandize bwanji ana anu kuti akhale ndi cholinga choti abatizidwe? Kodi achinyamata amene anabatizidwa komanso amene akufuna kubatizidwa angalimbitse bwanji ubwenzi wawo ndi Yehova?

28 Mbiri ya Moyo Wanga​—Ndinasiya Zinthu Zambiri Kuti Nditsatire Ambuye

32 Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2017

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena