Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w18 February tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
w18 February tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

MLUNGU WA APRIL 2-8, 2018

3 Tizikhala Okhulupirika Komanso Omvera Ngati Nowa, Danieli ndi Yobu

MLUNGU WA APRIL 9-15, 2018

8 Kodi Mumadziwa Yehova Ngati Mmene Nowa, Danieli ndi Yobu Ankamudziwira?

Nowa, Danieli ndi Yobu anakumana ndi mavuto ofanana ndi amene timakumana nawo masiku ano. Kodi n’chiyani chinawathandiza kudziwa bwino Yehova? Nanga n’chiyani chinawathandiza kuti akhalebe okhulupirika ndiponso omvera? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa.

13 Mbiri ya Moyo Wanga​—Zinthu Zonse N’zotheka ndi Yehova

MLUNGU WA APRIL 16-22, 2018

18 Kodi Kukhala Munthu Wauzimu Kumatanthauza Chiyani?

MLUNGU WA APRIL 23-29, 2018

23 Pitirizani Kukula Mwauzimu

Nkhani yoyamba ikufotokoza tanthauzo la munthu wauzimu komanso zimene tingaphunzire kwa anthu amene anasonyeza kuti ndi auzimu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene tingachite kuti tizikula mwauzimu komanso mmene kukhala munthu wauzimu kungatithandizire pa moyo wathu.

28 Chimwemwe Ndi Khalidwe Limene Mulungu Amapereka

31 Kale Lathu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena