Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w18 March tsamba 2
  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
w18 March tsamba 2

Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi

MLUNGU WA APRIL 30, 2018–MAY 6, 2018

3 Munthu Ayenera Kubatizidwa Kuti Akhale Mkhristu

MLUNGU WA MAY 7-13, 2018

8 Makolo, Kodi Mukuthandiza Ana Anu Kuti Ayenerere Kubatizidwa?

Kodi cholinga chathu tikamaphunzitsa anthu Baibulo chiyenera kukhala chiyani? N’chifukwa chiyani si nzeru kuzengereza kubatizidwa? N’chifukwa chiyani makolo ena amalimbikitsa ana awo kuti asabatizidwe msanga? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa komanso ena.

13 Mafunso Ochokera kwa Owerenga

MLUNGU WA MAY 14-20, 2018

14 Kuchereza Alendo Ndi Kofunika Kwambiri

Mtumwi Petulo anauza Akhristu a nthawi yake kuti: “Muzicherezana.” (1 Pet. 4:9) N’chifukwa chiyani tiyenera kutsatira kwambiri malangizo amenewa masiku ano? Nanga tingawatsatire m’njira ziti? Kodi tingatani ngati taitanidwa? Mafunso amenewa ayankhidwa munkhaniyi.

19 Mbiri ya Moyo Wanga—Yehova Sanandigwiritsepo Mwala!

MLUNGU WA MAY 21-27, 2018

23 Mulungu Amatilangiza Chifukwa Chotikonda

MLUNGU WA MAY 28, 2018–JUNE 3, 2018

28 “Mverani Malangizo Kuti Mukhale Anzeru”

Nkhanizi zikusonyeza kuti Yehova ndi Atate wathu amene amatipatsa malangizo kapena chilango chifukwa chotikonda. Koma kodi malangizo a Yehova amatithandiza bwanji? Nanga amapereka bwanji malangizo kapena chilango? Kodi ifeyo tiyenera kutani akatipatsa malangizo kapena chilango? Nanga tingatani kuti tikhale odziletsa? Nkhani ziwirizi ziyankha mafunso amenewa.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena