Nkhani Zimene Zili M’Magaziniyi
MLUNGU WA AUGUST 6-12, 2018
3 “Ufumu Wanga Suli Mbali ya Dziko Lino”
MLUNGU WA AUGUST 13-19, 2018
8 Tonsefe Tikhale Ogwirizana Ngati Yehova ndi Yesu
Anthu m’nthawi ya Yesu anali ogawikana chifukwa chosiyana pa nkhani ya ndale, maudindo komanso mitundu. Nkhani ziwirizi zikusonyeza zimene Yesu anaphunzitsa ophunzira ake kuti akhale ogwirizana ndiponso azipewa tsankho limene limagawanitsa anthu. Popeza anthu ambiri m’dzikoli sagwirizana, tionanso mmene chitsanzo cha ophunzirawo chingatithandizire.
13 Akanatha Kusangalatsa Mulungu
MLUNGU WA AUGUST 20-26, 2018
16 Muziphunzitsa Chikumbumtima Chanu ndi Malamulo Komanso Mfundo za Mulungu
Kuti chikumbumtima chathu chizititsogolera bwino tiyenera kuchiphunzitsa. Yehova watipatsa malamulo komanso mfundo zimene zingatithandize kuphunzitsa chikumbumtima chathu komanso kuona zinthu mmene iye amazionera. Nkhaniyi ikufotokoza mmene tingagwiritsire ntchito bwino mfundo za m’Baibulo.
MLUNGU WA AUGUST 27, 2018–SEPTEMBER 2, 2018
21 “Onetsani Kuwala Kwanu” Kuti Yehova Alemekezeke
Yesu anauza ophunzira ake kuti azionetsa kuwala kwawo kuti Mulungu alemekezeke. Nkhaniyi ikufotokoza zinthu zimene zingatithandize kuti tizionetsa kwambiri kuwala kwathu.
26 Mbiri ya Moyo Wanga—Ndakhala Ndikulimbikitsidwa pa Mavuto Anga Onse