Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse—Ku Myanmar
MLUNGU WA SEPTEMBER 3-9, 2018
7 Kodi Mumafuna Kukhala Wodziwika kwa Ndani?
Anthu ambiri amafuna kukhala odziwika m’dziko loipali. Munkhaniyi tikambirana zimene tingachite kuti tikhale odziwika kwa Yehova n’kumapeza madalitso amene iye amapereka kwa atumiki ake okhulupirika. Tionanso kuti nthawi zina anthu odziwika kwa Yehova amadalitsidwa m’njira imene sankayembekezera.
MLUNGU WA SEPTEMBER 10-16, 2018
12 Kodi Maso Anu Amayang’ana kwa Ndani?
Munkhaniyi tiona chifukwa chimene chinachititsa kuti Mose, yemwe anali wokhulupirika, alephere kulowa m’Dziko Lolonjezedwa. Tionanso mmene tingapewere zimene zinachitikira Mose.
MLUNGU WA SEPTEMBER 17-23, 2018
17 “Ndani Ali Kumbali ya Yehova?”
MLUNGU WA SEPTEMBER 24-30, 2018
Anthu onse padzikoli analengedwa ndi Yehova. Choncho tiyenera kukhala odzipereka kwa iye yekha. Anthu ena amanena kuti ndi okhulupirika kwa Mulungu koma kwinaku akuchita zinthu zosamumvera. Munkhani yoyamba tikambirana zimene tikuphunzira kwa Kaini, Solomo, Mose ndi Aroni. Munkhani yachiwiri tikambirana zimene tingachite posonyeza kuti timayamikira mwayi wokhala anthu a Yehova.
27 Muzichitira Chifundo Anthu “Kaya Akhale a Mtundu Wotani”
30 Kodi Mungatani Kuti Kuphunzira Baibulo Kuzikusangalatsani Komanso Kuzikuthandizani?