Nkhani Zimene Zili M’magaziniyi
3 Zimene Zinachitika Zaka 100 Zapitazo mu 1918
MLUNGU WA DECEMBER 3-9, 2018
6 Tizilankhula Zoona Zokhazokha
MLUNGU WA DECEMBER 10-16, 2018
11 Tiziphunzitsa Mfundo za Choonadi
Masiku ano anthu ambiri amakonda kunama. Koma kodi kunama kunayamba bwanji? Nanga bodza loipa kwambiri limene linanenedwapo ndi liti? Kodi tingapewe bwanji kupusitsidwa ndi anthu ena, nanga tingasonyeze bwanji kuti timalankhula zoona zokhazokha? Kodi Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa zingatithandize bwanji mu utumiki? Nkhanizi ziyankha mafunso onsewa.
17 Mbiri ya Moyo Wanga—Yehova Wandidalitsa Kwambiri Chifukwa cha Zimene Ndinasankha
MLUNGU WA DECEMBER 17-23, 2018
22 Tizikhulupirira Khristu Yemwe Ndi Mtsogoleri Wathu
MLUNGU WA DECEMBER 24-30, 2018
27 Tizikhalabe ndi Mtendere Wamumtima Zinthu Zikasintha
Popeza si ife angwiro, timavutika kuvomereza zinthu zikasintha pa moyo wathu kapena m’gulu la Yehova. Nkhani ziwirizi zitithandiza kuti tizikhala ndi mtendere wamumtima komanso tizidalira Mtsogoleri wathu Yesu Khristu ngakhale pamene zinthu pa moyo wathu zasintha mosayembekezereka.