Magazini Yophunzira
FEBRUARY 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: APRIL 8–MAY 5, 2019
© 2018 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI PATSAMBA LOYAMBA:
Yehova ankafuna kuti makolo azikonda ana awo komanso kuwaphunzitsa n’cholinga choti anawo azikhala otetezeka (Onani nkhani yophunzira 9, tsamba 7-8)