Magazini Yophunzira
JULY 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA KUYAMBIRA: SEPTEMBER 2-29, 2019
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI PATSAMBA LOYAMBA:
Abale ndi alongo ambiri amaganizira anthu ochokera kumayiko kumene sakhulupirira Yesu Khristu ndipo amawasonyeza malangizo othandiza omwe ali m’Baibulo (Onani nkhani yophunzira 30, ndime 12-13)