Magazini Yophunzira
NOVEMBER 2019
NKHANI ZOPHUNZIRA: DECEMBER 30, 2019–FEBRUARY 2, 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magaziniyi sitigulitsa. Timaipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwa kufuna kwawo. Ngati mukufuna kupereka pitani pa donate.jw.org.
Malemba onse m’magaziniyi akuchokera mu Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika lolembedwa m’Chichewa chamakono, kupatulapo ngati tasonyeza Baibulo lina.
CHITHUNZI CHAPACHIKUTO:
Pa Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo, mkulu wa ansembe ankalowa m’Malo Oyera Koposa atatenga zofukiza zonunkhira komanso makala amoto kuti malowo akhale ndi fungo labwino. Kenako ankalowanso m’malowo atatenga magazi a nsembe zamachimo (Onani nkhani yophunzira 47, ndime 4)