Nkhani Zimene Zatuluka Pa Jw Library Komanso Jw.Org
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Kuchita Zamatsenga Kuli ndi Vuto Lililonse?
Anthu ambiri amachita chidwi ndi zinthu monga ufiti komanso mavampaya. N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi ndi zoopsa?
Pa JW Library, pitani pamene alemba kuti PUBLICATIONS > ARTICLE SERIES > YOUNG PEOPLE ASK.
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.
KODI MUKUDZIWA?
Zimene Asayansi Afukula Zikutsimikizira Kuti Mfumu Davide Analikodi
Anthu ena amanena kuti Mfumu Davide ya ku Isiraeli sanali munthu weniweni. Koma kodi asayansi apeza zotani?
Pa jw.org, pitani pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > MBIRI KOMANSO BAIBULO > ZINTHU ZAKALE ZOSONYEZA KUTI BAIBULO NDI LOLONDOLA.