Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 11/97 tsamba 3
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—1997
Utumiki Wathu wa Ufumu—1997
km 11/97 tsamba 3

Zilengezo

◼ Mabuku ogaŵira mu November: Tidzapitiriza kugaŵira Uthenga wa Ufumu Na. 35. Mipingo imene iti itsirize kufola gawo lawo mwa kufikira eni nyumba ndi kope la Uthenga wa Ufumu Na. 35 panyumba iliyonse, ingagaŵire buku la Chidziŵitso. December: New World Translation ndi buku lakuti Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? January: Buku lililonse la masamba 192 lofalitsidwa 1985 isanafike lomwe mpingo uli nalo m’sitoko, Mipingo yomwe ilibe mabuku amenewo ingagaŵire buku lakuti Mungathe Kukhala ndi Moyo Kosatha m’Paradaiso pa Dziko Lapansi

February: Life—How Did It Get Here? By Evolution or by Creation? kapena Revelation—Its Grand Climax At Hand!

◼ Mkupiti wapaderawu utatha pa November 16, mipingo yomwe idzakhalabe ndi Uthenga wa Ufumu Na. 35 ingalimbikitse ofalitsa kugaŵa makope amenewo monga mmene amachitira ndi matrakiti, kaya kunyumba ndi nyumba kapena kwina kulikonse. Ngati mkhalidwe ukulola, ofalitsa angamasiye trakiti limodzi panyumba imene sanapezepo munthu, koma atatsimikiza kuti silionedwa ndi odutsa. Tiyesetsedi kugaŵira makope onse a uthenga wofunika umenewu.

◼ Mipingo ingayambe kuoda ma 1998 Yearbook of Jehovah’s Witnesses limodzi ndi oda yawo ya mabuku ya November. Ma Yearbook adzapezeka m’zinenero—pampambo umene tidzatumiza. Ma Yearbook ali zinthu zofuna oda yapadera ndipo pampambo wolongedzera mabuku a mpingo tidzalembapo kuti, “Zoyembekezeredwa,” kenako tidzakutumizirani.

◼ Zofalitsa Zomwe Zilipo:

Sangalalani ndi Moyo Padziko Lapansi Kosatha—Chicheŵa

Buku Lolangiza la Sukulu Yautumiki Wateokratiki—Chingelezi

Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja—Chingelezi

Kodi Chifuno cha Moyo Nchiyani—Kodi Mungachipeze Motani?—Chingelezi

◼ Makaseti Atsopano Omwe Alipo:

Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja—Chingelezi

◼ Mavidiyo Kaseti Atsopano Omwe Alipo:

The Bible—Its Power in Your Life (volyumu 3 pampambo wakuti The Bible—A Book of Fact and Prophecy)—Chingelezi

◼ Makompakiti Diski Atsopano Omwe Alipo:

◼ Kingdom Melodies No. 4

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena