Zilengezo
◼ Mabuku ogaŵira mu November: Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife? kapena Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha. December: Chidziŵitso Chotsogolera ku Moyo Wosatha. January: Buku lililonse la masamba 192 lofalitsidwa chaka cha 1986 chisanafike limene mpingo ungakhale nalo m’sitoko. February: Chinsinsi cha Chimwemwe cha Banja.
◼ Mipingo iyenera kuyamba kuoda ma Yearbook of Jehovah’s Witnesses a 2000 paoda yawo ya mabuku ya November. Ma Yearbook adzakhalapo m’Chingelezi. Mpaka pamene ma Yearbook adzakhalapo ndi kutumizidwa, adzaoneka ngati “Zoyembekezeredwa” pa ndandanda yolongedzera mabuku ya mipingo. Ma Yearbook ndi zinthu zaoda yapadera.
◼ Zofalitsa Zomwe Zilipo:
◼ Bokosi losungira magazini (Izi ndi za oda yapadera choncho oda iliyonse iyenera kutumizidwa ndi ndalama—C.W.O.)
◼ Pay Attention to Daniel’s Prophecy—Chingelezi
◼ Mabaundi voliyumu a 1998 a Watchtower ndi Awake!—Chingelezi (Izi ndi za oda yapadera choncho oda iliyonse iyenera kutumizidwa ndi ndalama—C.W.O.)
(Zapitirizidwa patsamba 8, danga 3)
Zilengezo(Zapitirizidwa)