Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 8/05 tsamba 7
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
Utumiki Wathu wa Ufumu—2005
km 8/05 tsamba 7

Zilengezo

◼ Mabuku ogawira mu July ndi August: Gawirani lililonse la mabulosha awa: Buku la Anthu Onse, Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu, Njira ya ku Moyo Wosatha—Kodi Mwaipeza?, ndi Sangalalani ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha! September: Gawirani buku la Lambirani Mulungu Woona Yekha. Mipingo imene ili ndi mabuku kapena mabulosha ambiri akale ingathe kugawira amenewo. Tikukumbutsanso mipingo kumaitanitsiratu mabuku okwanira ogwiritsa ntchito m’utumiki monga mmene Utumiki Wathu wa Ufumu uliwonse umasonyezera. October: Gawirani magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! Kwa amene aonetsa chidwi, asonyezeni bulosha la Mulungu Amafunanji. November: Gawirani buku la Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso. Ngati eninyumba akuoneka kuti alibe ana, gawirani buku la Chidziŵitso kapena thirakiti lakuti Kodi Mukufuna Kudziŵa Zambiri za Baibulo?

◼ Mwezi wa October ungadzakhale wabwino kuchita upainiya wothandiza chifukwa uli ndi mapeto a mlungu asanu athunthu.

◼ Nkhani zimene zili patsamba 6 mu Utumiki Wathu wa Ufumu uno muyenera kudzazigwiritsa ntchito pamene mukukonzekera pulogalamu ya tsiku la msonkhano wapadera wa chaka cha utumiki cha 2006.

◼ Woyang’anira wotsogolera kapena wina amene iye wam’sankha awerengere maakaunti a mpingo pa September 1 kapena patangodutsa masiku ochepa kuchokera pa detili. Akatha kuwerengerako, mukalengeze kumpingo mutamaliza kuwerenga lipoti lotsatira la maakaunti.

◼ Kuwerengera mabuku ndi magazini onse amene ali m’sitoko kumene kumachitika pachaka kuchitike pa August 31, 2005 kapena pakangodutsa masiku ochepa kuchokera pa detili. Kuwerengera kumeneku n’kofanana ndi kuwerengera mabuku kumene mtumiki wa mabuku amachita mwezi uliwonse, ndipo ziwerengero zonse zidzalembedwa pafomu ya Kuŵerengera Mabuku (S-18). Chiwerengero chonse cha magazini amene alipo mungachipeze kwa mtumiki wa magazini. Mlembi wa mpingo adzayang’anire kuwerengeraku. Iye pamodzi ndi woyang’anira wotsogolera adzasaine fomuyi. Mpingo uliwonse udzalandira mafomu atatu a Kuŵerengera Mabuku (S-18). Chonde tumizani pepala loyamba ku ofesi ya nthambi pasanadutse pa September 6. Sungani pepala lachiwiri m’faelo yanu. Pepala lachitatulo mungaligwiritse ntchito ngati powonkhetsera.

◼ Mipingo iyambe kuitanitsa Kalendala ya 2006 ya Mboni za Yehova, Kusanthula Malemba Tsiku ndi Tsiku—2006 ndi Yearbook of Jehovah’s Witnesses ya 2006 pa fomu yawo yotsatira yofunsira mabuku. Makalendala adzakhalapo m’Chichewa ndi Chingelezi. Mukhoza kuitanitsa mabuku a Kusanthula Malemba Tsiku ndi Tsiku m’Chichewa, Chingelezi ndi Chitumbuka. Yearbook idzakhalapo m’Chingelezi mokha basi.

◼ Zofalitsa Zatsopano Zomwe Zilipo:

Lambirani Mulungu Woona Yekha—Zilembo Zazikulu —Chichewa (wtlp-CN)

Samalani Ulosi wa Danieli! —Zilembo Zazikulu —Chichewa (dplp-CN)

Watch Tower Publications Index 2003—Chinenero Chamanja cha ku America (dxasl03-E)

Kusanthula Malemba Tsiku ndi Tsiku—2005 —Malifalensi a Chinenero Chamanja cha ku America (esasl05-E)

Njira ya ku Moyo Wosatha—Kodi Mwaipeza?—Chiyao

Mungathe Kukhala Bwenzi la Mulungu! —Chiyao

Yehova—Kodi Iye Ndani? (Thirakiti Na. 23)—Chiyao

Yesu Kristu—Kodi Iye Ndani? (Thirakiti Na. 24)—Chiyao

Does Fate Rule Our Lives?—Or Does God Hold Us Responsible? (Thirakiti Na. 71) —Chiyao

The Greatest Name (Thirakiti Na. 72)—Chiyao

Who Are Jehovah’s Witnesses? (Thirakiti Na. 73)—Chiyao

Hellfire—Is It Part of Divine Justice? (Thirakiti Na. 74) —Chiyao

◼ Madisiki Atsopano Omwe Alipo:

Warning Examples for Our Day —On Compact Disc —Chingelezi (cdwx-E)

Watchtower Library—2004 Edition—Chingelezi, —Chipwitikizi (Dziwani Izi: Kuyambira chaka chino izikhala ya chaka ndi chaka.)

Beware of Losing Faith By Drawing Away From Jehovah —On Compact Disc —Chingelezi (cdda-E)

Jehovah Delivers Those Calling Upon His Name—On Compact Disc—Chingelezi (cdcu-E)

Jehovah’s Judgment Against LawDefying People—On Compact Disc —Chingelezi (cdjj-E)

Keep Your Eye Simple— On Compact Disc —Chingelezi (cdey-E)

Families—Make Daily Bible Reading Your Way of Life! —On Compact Disc —Chingelezi (cdeb-E)

◼ Ma DVD Atsopano Omwe Alipo:

Album for The Watchtower Announcing Jehovah’s Kingdom —On DVD (2005)—Chinenero Chamanja cha ku America (dvdw05-E)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena