Zochitika Zosangalatsa za Muutumiki Wakumunda:
Ndife osangalala kukuuzani za kuwonjezeka kwa maphunziro a Baibulo amene tinachititsa mu September 2008. M’mweziwu tinachititsa maphunziro a Baibulo okwanira 69,835 ndipo chiwerengero chimenechi chaposa chiwerengero cha maphunziro a Baibulo omwe tinachititsa mu September 2007 ndi anthu okwana 904.