Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • km 6/11 tsamba 4
  • Zilengezo

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zilengezo
  • Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
km 6/11 tsamba 4

Zilengezo

◼ Mabuku ogawira m’mwezi wa June: Gawirani buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo pa ulendo woyamba. Ngati mwininyumba ali nalo kale bukuli ndipo sakufuna kuti muyambe kuphunzira naye Baibulo, mungam’patse magazini yakale kapena kabuku kamene angachite nako chidwi. July ndi August: Gawirani kabuku kalikonse kamasamba 32 kamene anthu angachite nako chidwi m’gawo lanu monga: Boma Limene Lidzabweretsa Paradaiso, Dikirani!, Kodi Mulungu Amatisamaliradi?, Mizimu ya Akufa—Kodi Ingakuthandizeni Kapena Kukuvulazani? Kodi Iyo Ilikodi?, Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, Sangalalani Ndi Moyo pa Dziko Lapansi Kosatha! ndi kakuti, “Tawonani! Ndikupanga Zinthu Zonse Zatsopano”. September: Gawirani buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Yesetsani kuyambitsa maphunziro a Baibulo pa ulendo woyamba. Ngati mwininyumba ali nalo kale bukuli ndipo sakufuna kuti muyambe kuphunzira naye Baibulo, mungam’patse magazini yakale kapena kabuku kamene angachite nako chidwi.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena