Zochitika mu Utumiki Wakumunda
M’chaka chautumiki cha 2012, abale ndi alongo okwana 3,218 anabatizidwa posonyeza kudzipereka kwawo kwa Yehova. Tiyeni tipitirize kuthandiza anthu ‘onse amene ali ndi maganizo abwino kuti adzapeze moyo wosatha.’ Tiyeni tichite zimenezi makamaka pa nyengo ino ya Chikumbutso.—Mac. 13:48.