Zilengezo
◼ Mabuku ogawira mu October: Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! November ndi December: Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? kapena kapepala kakuti, Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? January 2015: Kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu.