Zochitika mu Utumiki Wakumunda
Pa nthawi yomwe tinkagwira ntchito yoitanira anthu ku Chikumbutso chaka chino, abale ndi alongo 5,969 anachita upainiya wothandiza m’mwezi wa March ndipo abale ndi alongo okwana 6,321 anachita upainiya wothandiza mu April. Zimene tinachita m’miyezi imeneyi zinathandiza kuti Yehova Mulungu atamandidwe.—Sal. 106:1.