Zochitika mu Utumiki Wakumunda
Chaka chatha tinachititsa maphunziro a Baibulo 113, 332. Izi zikusonyeza kuti m’gawo la nthambi yathu muli anthu ambiri amene tifunika kuwathandiza mapeto asanafike. (Mat. 28:19, 20) Choncho, tiyeni tipitirize kuthandiza anthu a mitima yabwino amenewa kuti ayambe kutumikira Yehova.