Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsamba 2
  • February 1-7

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • February 1-7
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 February tsamba 2

February 1-7

NEHEMIYA 1-4

  • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nehemiya Ankakonda Kulambira Yehova”: (10 min.)

    • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Nehemiya.]

    • Neh. 1:11; 2:1-3—Nehemiya ankasangalala chifukwa cholambira Yehova (w06 2/1 9 ndime 7)

    • Neh. 4:14—Nehemiya anadalira Yehova pamene ankatsutsidwa (w06 2/1 10 ndime 3)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Neh. 1:1; 2:1—Kodi tikudziwa bwanji kuti chaka cha 20 chotchulidwa pa Nehemiya 1:1 n’chofanana ndi chotchulidwa pa Nehemiya 2:1? (w06 2/1 8 ndime 5)

    • Neh. 4:17, 18—Kodi zinkatheka bwanji kumanga ndi dzanja limodzi? (w06 2/1 9 ndime 1)

    • Kodi ndaphunzira chiyani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Neh. 3:1-14 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Konzekerani Zitsanzo za Ulaliki za Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani kavidiyo kosonyeza zitsanzo za ulaliki kenako kambiranani mfundo zimene mwaphunzirapo. Fotokozani zimene wofalitsa wachita kuti adzapange ulendo wobwereza. Limbikitsani omvera kuti alembe ulaliki umene angakonde kugwiritsa ntchito.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 103

  • Konzani Zoti Mudzachite Upainiya Wothandiza M’mwezi wa March Kapena April: (15 min.) Nkhani yokambirana. Gwiritsani ntchito mfundo zimene zili m’nkhani yakuti, “Zimene Mungachite Kuti Mudzasangalale M’nyengo ya Chikumbutso.” (km 2/14 2) Limbikitsani omvera kuti ayambe kukonzekera. (Miy. 21:5) Kenako funsani ofalitsa awiri amene anachitapo upainiya wothandiza kuti afotokoze mavuto amene anapirira komanso zosangalatsa zimene anapeza?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 25 ndime 9-16 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena