Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsamba 4
  • Moyo Wabwino Kwambiri

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Moyo Wabwino Kwambiri
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulira?—Gawo 1
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulira?—Gawo 2
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Mmene Tingafotokozere Zimene Timakhulupirira Zokhudza Chaka cha 1914
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Zamkatimu
    Galamukani!—2013
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 February tsamba 4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Moyo Wabwino Kwambiri

Achinyamata akhoza kuchita zambiri m’gulu la Yehova. Onerani vidiyo yakuti Moyo Wabwino Kwambiri, kuti muone zinthu zabwino zimene mtsikana wina dzina lake Cameron wachita. Kenako yankhani mafunso ali m’munsiwa. (Pitani pa jw.org/ny, pamene alemba kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA.)

Cameron akusonyeza mmene anayendera pochoka ku United States kupita ku Malawi
  • Kodi Cameron amaona kuti chofunika kwambiri pamoyo wake n’chiyani?

  • Kodi anawonjezera liti utumiki wake nanga anachita bwanji zimenezi?

  • Kodi anakonzekera bwanji kukatumikira kudziko limene kukufunika olalikira ambiri?

    Cameron akusonyeza mmene anayendera pochoka ku United States kupita ku Malawi
  • Kodi ndi mavuto ati amene anakumana nawo kudziko limene anapita?

  • Kodi kulalikira kudera lachilendo kuli ndi ubwino wotani?

  • Kodi Cameron wadalitsidwa bwanji?

    A Mboni ku Malawi akupereka moni
  • N’chifukwa chiyani tinganene kuti munthu amene akutumikira Yehova amakhala ndi moyo wabwino kwambiri?

  • Kodi ndi zinthu zina ziti zimene achinyamata angachite m’gulu la Yehova?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena