CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | NEHEMIYA 12-13
Zimene Tikuphunzira kwa Nehemiya
Nehemiya anali wakhama poteteza kulambira koona
Mkulu wa ansembe dzina lake Eliyasibu analola kuyendera maganizo a Tobiya, yemwe sankalambira Yehova
Eliyasibu anakonzera Tobiya chipinda m’bwalo la nyumba ya Mulungu
Nehemiya anataya kunja katundu wa Tobiya n’kuyeretsa chipindacho kuti chizigwira ntchito yake yoyenera
Nehemiya anapitiriza kuyeretsa Yerusalemu