Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsamba 5
  • April 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • April 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 April tsamba 5

April 18-24

YOBU 28-32

  • Nyimbo Na. 17 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yobu Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kukhala ndi Mtima Wosagawanika”: (10 min.)

    • Yobu 31:1—Yobu anachita “pangano” ndi maso ake (w15 6/15 16 ndime 13; w15 1/15 25 ndime 10)

    • Yobu 31:13-15—Yobu anali wodzichepetsa, wachilungamo ndiponso wachifundo (w10 11/15 30 ndime 8-9)

    • Yobu 31:16-25—Yobu anali woolowa manja kwa anthu ovutika (w10 11/15 30 ndime 10-11)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 32:2—Kodi Yobu anasonyeza bwanji kuti ankadziona kuti iyeyo “anali wolungama, osati Mulungu”? (w15 7/1 12 ndime 2; it-1-E 606 ndime 5)

    • Yobu 32:8, 9—N’chifukwa chiyani Elihu anaona kuti ayankhule ngakhale kuti anali mwana kwa Yobu ndi anzake ena? (w06 3/15 16 ndime 1; it-2-E 549 ndime 6)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: Yobu 30:24–31:14 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: g16.2 12-13—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira. (Osapitirira 2 min.)

  • Ulendo Wobwereza: g16.2 12-13—Muuzeni nkhani imene mudzaphunzire ulendo wotsatira. (Osapitirira 4 min.)

  • Phunziro la Baibulo: bh 148 ndime 8-9 (Osapitirira 6 min.)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 115

  • Tingaphunzire Zambiri kwa Anthu Amene Anasonyeza Mtima Wosagawanika (1 Pet. 5:9): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya mutu wakuti, Harold King Anakhalabe Wokhulupirika M’ndende (Vidiyo imeneyi ikupezeka pa jw.org pambali yakuti Zofalitsa Nkhani pa akaunti ya mpingo wanu.) Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi n’chiyani chinathandiza M’bale King kuti asasiye kutumikira Yehova pamene anali m’ndende? Kodi kuimba nyimbo za Ufumu kungatithandize bwanji kupirira tikamakumana ndi mavuto? Kodi zimene M’bale King anachita zakulimbikitsani bwanji?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 29 ndime 1-10 (30 min.)

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 81 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena