Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsamba 2
  • May 2-8

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • May 2-8
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 May tsamba 2

May 2-8

YOBU 38-42

  • Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amasangalala Tikamapempherera Ena”: (10 min.)

    • Yobu 42:7, 8—Yehova ankayembekezera kuti Yobu apempherere Elifazi, Bilidadi ndi Zofari (w13 6/15 21 ndime 17; w98 5/1 30 ndime 3-6)

    • Yobu 42:10—Yobu atawapempherera, Yehova anamupatsanso moyo wathanzi ngati mmene analili poyamba (w98 5/1 31 ndime 3)

    • Yobu 42:10-17—Yehova anadalitsa kwambiri Yobu chifukwa chakuti anali ndi chikhulupiriro komanso anali wopirira (w94 11/15 20 ndime 19-20)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Yobu 38:4-7—Kodi “nyenyezi za m’mawa” ndi ndani, nanga tikudziwa zotani zokhudza iwowo? (bh 97 ndime 3)

    • Yobu 42:3-5—Kodi ifeyo tingatani kuti tiziona Mulungu ngati mmene Yobu anachitira? (w15 10/15 8 ndime 16-17)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yobu 41:1-26

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse payokha, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo. Kenako pokambirana mmene tingagwiritsire ntchito chipangizo chamakono, tchulani mwachidule mfundo za m’nkhani yakuti, “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW.” Kumbutsani ofalitsa kuti kumapeto kwa mwezi uliwonse asamaiwale kulemba lipoti la maulendo omwe anaonetsako munthu vidiyo mu utumiki. Limbikitsani ofalitsa kuti alembe ulaliki wawowawo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 60

  • “Kodi Mumagwiritsa Ntchito Laibulale ya JW?”: (15 min.) Yambani ndi kukambirana nkhaniyi kwa maminitsi 5. Kenako onetsani ndi kukambirana mwachidule mfundo za mu vidiyo yakuti Yambani Kugwiritsa Ntchito “Laibulale ya JW.” Chitaninso chimodzimodzi ndi mavidiyo akuti Pangani Dawunilodi Mabuku ndi Sinthani Zinthu Zina Kuti Muone Zimene Mukufuna Powerenga. Pomaliza limbikitsani ofalitsa onse omwe angathe kuti apange dawunilodi Laibulale ya JW. Alimbikitseni kuti achite zimenezi usanafike mlungu wa May 16, womwe mudzakambirane nkhani yakuti, “Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW.”

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 29 ndime 16-21, ndi bokosi patsamba 299

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 77 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena