Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsamba 5
  • August 15-21

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 15-21
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 August tsamba 5

August 15-21

MASALIMO 102-105

  • Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi”: (10 min.)

    • Sal. 103:8-12—Yehova ndi wachifundo kwambiri moti amatikhululukira tikalapa (w13 6/15 20 ndime 14; w12 7/15 16 ndime 17)

    • Sal. 103:13, 14—Yehova amadziwa zinthu zimene sitingakwanitse kuchita (w15 4/15 26 ndime 8; w13 6/15 15 ndime 16)

    • Sal. 103:19, 22—Tiziyamikira chifundo chimene Yehova amatisonyeza poyesetsa kuchita zimene amafuna (w10 11/15 25 ndime 5; w07 12/1 21 ndime 1)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 102:12, 27—Kodi kuganizira kwambiri za ubwenzi wathu ndi Yehova kungatithandize bwanji tikakhumudwa? (w14 3/15 16 ndime 19-21)

    • Sal. 103:13—N’chifukwa chiyani nthawi zina Yehova sayankha mapemphero athu nthawi yomweyo? (w15 4/15 25 ndime 7)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 105:24-45

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g16.4 tsamba 10-11—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g16.4 tsamba 10-11—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 164-166 ndime 3-4—Muthandizeni kuona mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 91

  • Osaiwala Zinthu Zonse Zimene Yehova Wakuchitirani (Sal. 103:1-5): (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yamutu wakuti, Khalidwe Langa Loipa Linanditopetsa. (Imapezeka pa jw.org/ny pamene palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZIMENE TIMACHITA.) Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi tili ndi zifukwa zotani zotamandira Yehova? Kodi tikuyembekezera madalitso otani chifukwa cha ubwino wa Yehova?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 4 ndime 16-31 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 41.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena