Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsamba 6
  • August 22-28

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • August 22-28
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 August tsamba 6

August 22-28

MASALIMO 106-109

  • Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muziyamikira Yehova”: (10 min.)

    • Sal. 106:1-3—Yehova ndi woyenera kumuthokoza (w15 1/15 8 ndime 1; w02 6/1 18 ndime 19)

    • Sal. 106:7-14, 19-25, 35-39—Aisiraeli anasiya kuthokoza Yehova ndipo sanakhalenso okhulupirika (w15 1/15 8-9 ndime 2-3; w01 6/15 13 ndime 1-3)

    • Sal. 106:4, 5, 48—Tili ndi zifukwa zambiri zothokozera Yehova (w11 10/15 5 ndime 7; w03 12/1 15-16 ndime 3-6)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Sal. 109:8—Kodi Mulungu anakonzeratu zoti Yudasi apereke Yesu kuti ulosi ukwaniritsidwe? (w00 12/15 24 ndime 20; it-1-E 857-858)

    • Sal. 109:31—Kodi Yehova amaima bwanji “kudzanja lamanja la munthu wosauka”? (w06 9/1 14 ndime 8)

    • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 106:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) ll 6—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) ll 7—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 178-179 ndime 14-16—Muthandizeni wophunzirayo kuona mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 94

  • Yehova Adzatisamalira (Sal. 107:9): (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti, Yehova Adzatisamalira. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BANJA.) Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 5 ndime 1-13.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena